Tithandizane
Za Makina aKompiyuta
Ngati
mukufuna kuti ndikuthandizeni zakompiyuta, ndili okonzeka
kutero mumagawo ngati awa: kumphunzitsa ana asukulu kapena
ena omwe akugwira kale ntchito, ntchito zina ngati kukonza
malo ngati ano, ndi zina zomwe mungafune. ndili okonzekanso
kukuthandizani ngati mukufuna kupanga mfundo panthawi yomwe
mukufuna kugula makina ndi zina zokhuzana ndi kompiyuta.
Ntchito
ngati zimenezi ndimalipilitsa ndipo nthawi zina zimakhala
zaulele.
Ngati
mukufuna kudziwa zambiri kapena muli ndi gawo lomwe mukufuna
ndizathandizepo, ndiuzeni.
|