Ndakulandilani, Welcome, Karibu, Welkom, Youkoso, Namaste, Bem-vindo, Bienvenida, Assalam-o-alaikum!, Bienvenue
Patsinde
Dziwani Zaine
Tithandizane
Malo Ena
Zogawana

Kunyadila zachiMalawi

Dziwawani za malonje ena ochokera maiko ena.

Ndakulandilani, Welcome, Karibu, Bienvenue

Takulandilani kuno ku kkps omwe ndikhulupilira kuti akhalanso malo anu pomwe mudzatha kugawana nane zina ndi zina. Ndicholinga changa kuti malo ano athe kufikila kwaiwo omwe akufuna kudziwa kumene zamakina a kompiyuta ndikwaena odziwa kale pofuna kupititsa patsogolo chitukuko cha dziko lathu la Malawi. Ndikufunirani zonse zabwino ndipo ndigawilerni maganizo anu kuti ndithe kukutumikilani bwino.


Ukadawulo wa atsogoleri - Maganizo atsogoleri otchuka kwambiri padziko lapansi. Zolembedwa ndi Pravin Rajpal.

Maganizo anu ndi otani pazamavuto aku Zimbabwe ndi Malawi? Ena akuti kuthetsa mavuto aku Zimbabwe nkovuta kwambiri ndipo aku Malawi, nkosavuta. Inu mukuti chani pankhaniyi? Ndigawireni maganizo anu.
Pulezidenti Mugabe  Pulezidenti Mutharika 
Kodi utsogoleri ndi chani?

English

TIGAWANE ZA MAPHUNZIRO A KOMPIYUTA

SPSS for Windows

Epi Info

Sage Line 50 

MS Office - Word, Excel, Access, FrontPage

OpenOffice

Zotetezedwa © 2001 - 2008 Tasha Communications

Zolembedwa zonse ndizotetezedwa. Muli ololedwa kugwiritsa ntchito magawo onse amalo ano posasowa chilolezo china chili chonse koma mukupemphedwa kunena komwe mwazitenga ku Tasha Communications.

Hosted by www.Geocities.ws

1